-
Danieli 12:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Anthu ambiri amene agona munthaka adzadzuka. Ena adzalandira moyo wosatha koma ena adzachititsidwa manyazi komanso adzadedwa mpaka kalekale.
-