-
Danieli 12:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Anthu ozindikira adzawala kwambiri ngati kuwala kwa kuthambo. Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kuti akhale olungama adzawala ngati nyenyezi mpaka muyaya.
-