Danieli 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno ineyo Danieli nditayangʼana, ndinaona angelo ena awiri ataimirira. Mngelo mmodzi anaima mʼmbali mwa mtsinje tsidya lino ndipo wina anaima tsidya linalo.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:5 Ulosi wa Danieli, tsa. 294
5 Ndiyeno ineyo Danieli nditayangʼana, ndinaona angelo ena awiri ataimirira. Mngelo mmodzi anaima mʼmbali mwa mtsinje tsidya lino ndipo wina anaima tsidya linalo.+