Danieli 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ine ndinamva zimene ananenazo, koma sindinadziwe tanthauzo lake.+ Choncho ndinafunsa kuti: “Inu mbuyanga, kodi zinthu zimenezi zidzatha bwanji?” Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:8 Ulosi wa Danieli, ptsa. 296-297
8 Tsopano ine ndinamva zimene ananenazo, koma sindinadziwe tanthauzo lake.+ Choncho ndinafunsa kuti: “Inu mbuyanga, kodi zinthu zimenezi zidzatha bwanji?”