Danieli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwe, ndiponso pamene chinthu chonyansa chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwe,+ padzadutsa masiku 1,290. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:11 Ulosi wa Danieli, ptsa. 297-301 Nsanja ya Olonda,11/1/1993, ptsa. 10-11
11 Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwe, ndiponso pamene chinthu chonyansa chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwe,+ padzadutsa masiku 1,290.