Hoseya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mayiyu adzathamangira amuna omukonda kwambiriwo, koma sadzawapeza.+Adzawafunafuna, koma osawapeza. Ndiyeno adzanena kuti, ‘Ndibwerera kwa mwamuna wanga woyamba,+Chifukwa zinthu zinkandiyendera bwino nthawi imeneyo kusiyana ndi pano.’+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 19
7 Mayiyu adzathamangira amuna omukonda kwambiriwo, koma sadzawapeza.+Adzawafunafuna, koma osawapeza. Ndiyeno adzanena kuti, ‘Ndibwerera kwa mwamuna wanga woyamba,+Chifukwa zinthu zinkandiyendera bwino nthawi imeneyo kusiyana ndi pano.’+