Hoseya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ndinamuuza kuti: “Ukhala wanga masiku ambiri. Usachite uhule* ndipo usagone ndi mwamuna wina. Inenso sindigona nawe.” Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, ptsa. 19-20
3 Ndiyeno ndinamuuza kuti: “Ukhala wanga masiku ambiri. Usachite uhule* ndipo usagone ndi mwamuna wina. Inenso sindigona nawe.”