Hoseya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Tamvani izi inu ansembe,+Ndipo mvetserani inu a mʼnyumba ya Isiraeli.Inunso a mʼnyumba ya mfumu mvetserani,Popeza chiweruzochi chikukhudza inuyo,Chifukwa mwakhala msampha ku MizipaNdiponso ngati ukonde paphiri la Tabori.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, tsa. 1611/15/2005, tsa. 213/1/1989, tsa. 14
5 “Tamvani izi inu ansembe,+Ndipo mvetserani inu a mʼnyumba ya Isiraeli.Inunso a mʼnyumba ya mfumu mvetserani,Popeza chiweruzochi chikukhudza inuyo,Chifukwa mwakhala msampha ku MizipaNdiponso ngati ukonde paphiri la Tabori.+