Hoseya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Efuraimu waponderezedwa ndi chiweruzo,Chifukwa anatsimikiza mtima kutsatira mdani wake.+