Hoseya 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndinali ngati njenjete* kwa Efuraimu,Ndipo ndinachititsa kuti nyumba ya Yuda iwole.