Hoseya 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako ndidzabwerera kumalo anga mpaka iwo atakumana ndi zotsatira za zolakwa zawo,Ndipo adzayamba kundifunafuna kuti ndiwakomere mtima.+ Akadzakumana ndi mavuto, adzandifuna.”+
15 Kenako ndidzabwerera kumalo anga mpaka iwo atakumana ndi zotsatira za zolakwa zawo,Ndipo adzayamba kundifunafuna kuti ndiwakomere mtima.+ Akadzakumana ndi mavuto, adzandifuna.”+