-
Hoseya 6:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 “Kodi ndikuchite chiyani iwe Efuraimu?
Nanga iwe Yuda, ndikuchite chiyani?
Chifukwa chikondi chanu chokhulupirika chili ngati mitambo yamʼmawa,
Ndiponso ngati mame amene sachedwa kuuma.
-