Hoseya 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Giliyadi ndi tauni ya anthu ochita zoipa,+Yodzaza ndi zidindo za mapazi amagazi.+