Hoseya 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Nthawi zonse ndikafuna kuchiritsa Isiraeli,Zolakwa za Efuraimu zimaonekera,+Ndiponso zoipa za Samariya.+ Chifukwa iwo amachita zachinyengo.+Anthu akuba amathyola nyumba ndipo gulu la achifwamba limasakaza panja.+
7 “Nthawi zonse ndikafuna kuchiritsa Isiraeli,Zolakwa za Efuraimu zimaonekera,+Ndiponso zoipa za Samariya.+ Chifukwa iwo amachita zachinyengo.+Anthu akuba amathyola nyumba ndipo gulu la achifwamba limasakaza panja.+