Hoseya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsoka kwa iwo chifukwa andithawa! Adzawonongedwa chifukwa andilakwira. Ndinali wokonzeka kuwawombola, koma andinamizira mabodza.+
13 Tsoka kwa iwo chifukwa andithawa! Adzawonongedwa chifukwa andilakwira. Ndinali wokonzeka kuwawombola, koma andinamizira mabodza.+