Hoseya 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wina adzapita nalo kudziko la Asuri nʼkukalipereka ngati mphatso kwa mfumu yaikulu.+ Efuraimu adzachititsidwa manyazi,Ndipo Isiraeli adzachita manyazi chifukwa cha malangizo amene ankatsatira.+
6 Wina adzapita nalo kudziko la Asuri nʼkukalipereka ngati mphatso kwa mfumu yaikulu.+ Efuraimu adzachititsidwa manyazi,Ndipo Isiraeli adzachita manyazi chifukwa cha malangizo amene ankatsatira.+