Hoseya 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Samariya pamodzi ndi mfumu yake adzawonongedwa,*+Ngati kanthambi kothyoledwa mumtengo kamene kakuyandama pamadzi. Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:7 Yesaya 1, ptsa. 320-321 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, ptsa. 26-27
7 Samariya pamodzi ndi mfumu yake adzawonongedwa,*+Ngati kanthambi kothyoledwa mumtengo kamene kakuyandama pamadzi.