Hoseya 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Efuraimu anali ngʼombe* yophunzitsidwa bwino yokonda kupuntha mbewu,Choncho ine sindinawononge khosi lake lokongola. Koma ndidzachititsa kuti wina akwere pamsana pa Efuraimu.+ Yuda adzalima, Yakobo adzamusalazira zibulumwa za dothi.
11 Efuraimu anali ngʼombe* yophunzitsidwa bwino yokonda kupuntha mbewu,Choncho ine sindinawononge khosi lake lokongola. Koma ndidzachititsa kuti wina akwere pamsana pa Efuraimu.+ Yuda adzalima, Yakobo adzamusalazira zibulumwa za dothi.