Hoseya 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinkawakoka mokoma mtima ndiponso mwachikondi,*+Kwa iwo ndinali ngati wochotsa goli mʼkhosi* mwawo,Ndipo mwachikondi ndinkabweretsera aliyense chakudya. Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:4 Tsiku la Yehova, ptsa. 133-134 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 2811/1/2005, tsa. 21
4 Ndinkawakoka mokoma mtima ndiponso mwachikondi,*+Kwa iwo ndinali ngati wochotsa goli mʼkhosi* mwawo,Ndipo mwachikondi ndinkabweretsera aliyense chakudya.