-
Yoweli 1:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iwo awononga mtengo wanga wa mpesa ndipo asandutsa mtengo wanga wa mkuyu kukhala chitsa.
Nthambi za mitengoyi azichotsa makungwa nʼkuzitaya.
Mphukira zake azichotsanso makungwa.
-