Yoweli 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nsembe zambewu+ ndi nsembe zachakumwa+ sizikupezekanso mʼnyumba ya Yehova.Ansembe omwe ndi atumiki a Yehova, akulira. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, tsa. 10
9 Nsembe zambewu+ ndi nsembe zachakumwa+ sizikupezekanso mʼnyumba ya Yehova.Ansembe omwe ndi atumiki a Yehova, akulira.