-
Yoweli 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Alimi asokonezeka ndipo osamalira minda ya mpesa akulira mofuula,
Chifukwa cha tirigu ndi barele.
Popeza zokolola zamʼmunda zawonongeka.
-