Yoweli 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsikulo lidzakhala lochititsa mantha. Tsiku la Yehova lili pafupi.+Lidzafika ngati chiwonongeko chochokera kwa Wamphamvuyonse. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:15 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, tsa. 11
15 Tsikulo lidzakhala lochititsa mantha. Tsiku la Yehova lili pafupi.+Lidzafika ngati chiwonongeko chochokera kwa Wamphamvuyonse.