-
Yoweli 1:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kodi chakudya sichinachotsedwe ife tikuona?
Kodi kusangalala sikunachotsedwe mʼnyumba ya Mulungu wathu?