Yoweli 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mbewu* zawonongeka mafosholo ali pamwamba pake. Nyumba zosungiramo zinthu zawonongedwa. Nkhokwe zapasulidwa chifukwa mbewu zauma.
17 Mbewu* zawonongeka mafosholo ali pamwamba pake. Nyumba zosungiramo zinthu zawonongedwa. Nkhokwe zapasulidwa chifukwa mbewu zauma.