Yoweli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amadumphadumpha ndipo amachita mkokomo ngati magaleta oyenda pamwamba pa mapiri,+Ndiponso ngati moto walawilawi umene ukutentha mapesi. Ali ngati anthu amphamvu omwe ayalana pokonzekera kumenya nkhondo.+
5 Amadumphadumpha ndipo amachita mkokomo ngati magaleta oyenda pamwamba pa mapiri,+Ndiponso ngati moto walawilawi umene ukutentha mapesi. Ali ngati anthu amphamvu omwe ayalana pokonzekera kumenya nkhondo.+