-
Yoweli 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Iwo amathamangira mʼmizinda ndipo amathamanga pakhoma la mpanda.
Amakwera nyumba ndipo amalowera pawindo ngati mbala.
-