Yoweli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzawalankhula asilikali ake mokweza+ chifukwa anthu amumsasa wake ndi ambiri.+ Amene akukwaniritsa mawu ake ndi wamphamvu.Tsiku la Yehova ndi lalikulu komanso lochititsa mantha.+ Ndani angalimbe pa tsiku limeneli?”+ Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 9, 1212/15/1997, tsa. 11
11 Yehova adzawalankhula asilikali ake mokweza+ chifukwa anthu amumsasa wake ndi ambiri.+ Amene akukwaniritsa mawu ake ndi wamphamvu.Tsiku la Yehova ndi lalikulu komanso lochititsa mantha.+ Ndani angalimbe pa tsiku limeneli?”+