Yoweli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngʼambani mitima yanu,+ osati zovala zanu,+Ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu,Chifukwa iye ndi wachifundo, wokoma mtima, wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka.+Iye adzasintha maganizo okubweretserani tsoka. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:13 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 15-163/15/1989, tsa. 30
13 Ngʼambani mitima yanu,+ osati zovala zanu,+Ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu,Chifukwa iye ndi wachifundo, wokoma mtima, wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka.+Iye adzasintha maganizo okubweretserani tsoka.