Yoweli 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sonkhanitsani anthu ndipo muyeretse mpingo.+ Sonkhanitsani amuna achikulire,* ana komanso makanda.+ Mkwati atuluke mʼchipinda chake ndipo nayenso mkwatibwi atuluke mʼchipinda chake. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Tsiku la Yehova, tsa. 137
16 Sonkhanitsani anthu ndipo muyeretse mpingo.+ Sonkhanitsani amuna achikulire,* ana komanso makanda.+ Mkwati atuluke mʼchipinda chake ndipo nayenso mkwatibwi atuluke mʼchipinda chake.