-
Yoweli 2:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mdani wakumpoto ndidzamuthamangitsira kutali ndi inu.
Ndidzamuthamangitsira kudziko louma komanso lopanda anthu,
Nkhope yake itayangʼana kunyanja yakumʼmawa,*
Nkhongo yake italoza kunyanja yakumadzulo.*
Fungo lake lonunkha lidzamveka,
Ndipo fungo lake loipalo lidzafalikira mʼdziko lonselo,+
Chifukwa Mulungu adzachita zinthu zazikulu.’
-