Yoweli 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Malo opunthira mbewu adzadzaza ndi mbewu,Ndipo malo opangira vinyo komanso mafuta adzasefukira.+ Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:24 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 17-18