Yoweli 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mudzadya nʼkukhuta,+Ndipo mudzatamanda dzina la Yehova Mulungu wanu,+Amene wakuchitirani zodabwitsa.Anthu anga sadzachitanso manyazi mpaka kalekale.+
26 Mudzadya nʼkukhuta,+Ndipo mudzatamanda dzina la Yehova Mulungu wanu,+Amene wakuchitirani zodabwitsa.Anthu anga sadzachitanso manyazi mpaka kalekale.+