-
Yoweli 3:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Sulani makasu anu a pulawo kuti akhale malupanga, ndiponso zida zanu zosadzira mitengo kuti zikhale mikondo.
Munthu wofooka anene kuti: “Ndine wamphamvu.”
-