Yoweli 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu anthu a mitundu yotizungulira, bwerani mudzathandize ndipo nonse musonkhane.’”+ Inu Yehova, bweretsani asilikali anu kumalo amenewo. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 23-24
11 Inu anthu a mitundu yotizungulira, bwerani mudzathandize ndipo nonse musonkhane.’”+ Inu Yehova, bweretsani asilikali anu kumalo amenewo.