Yoweli 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yambani kumweta ndi chikwakwa, chifukwa zokolola zacha. Bwerani nʼkuyamba kuponda chifukwa moponderamo mphesa mwadzaza.+ Malo ogweramo vinyo asefukira, chifukwa zoipa zawo zachuluka kwambiri. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 284 Nsanja ya Olonda,5/1/1992, tsa. 95/15/1987, ptsa. 18-19
13 Yambani kumweta ndi chikwakwa, chifukwa zokolola zacha. Bwerani nʼkuyamba kuponda chifukwa moponderamo mphesa mwadzaza.+ Malo ogweramo vinyo asefukira, chifukwa zoipa zawo zachuluka kwambiri.