Amosi 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinachititsa ana anu ena kukhala aneneri.+Ndipo anyamata anu ena ndinawachititsa kukhala Anaziri.+ Si choncho kodi, inu Aisiraeli?’ watero Yehova.
11 Ndinachititsa ana anu ena kukhala aneneri.+Ndipo anyamata anu ena ndinawachititsa kukhala Anaziri.+ Si choncho kodi, inu Aisiraeli?’ watero Yehova.