Amosi 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Perekani nsembe zoyamikira za mkate wokhala ndi zofufumitsa.+Ndipo lengezani mokweza za nsembe zanu zaufulu! Chifukwa nʼzimene mumakonda kuchita, inu Aisiraeli,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
5 Perekani nsembe zoyamikira za mkate wokhala ndi zofufumitsa.+Ndipo lengezani mokweza za nsembe zanu zaufulu! Chifukwa nʼzimene mumakonda kuchita, inu Aisiraeli,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.