Amosi 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu amʼmizinda iwiri kapena itatu anayenda movutikira kupita mumzinda wina kuti akamwe madzi,+Ndipo ludzu lawo silinathe,Koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.
8 Anthu amʼmizinda iwiri kapena itatu anayenda movutikira kupita mumzinda wina kuti akamwe madzi,+Ndipo ludzu lawo silinathe,Koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.