-
Amosi 5:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 ‘Namwali, Isiraeli, wagwa.
Iye sangathenso kuimirira.
Aliyense wamuthawa nʼkumusiya mʼdziko lake.
Ndipo palibe womudzutsa.’
-