-
Amosi 5:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, Yehova wanena kuti:
‘Padzamveka kulira mʼmabwalo onse a mizinda yanu,
Ndipo mʼmisewu yanu yonse anthu azidzati: “Mayo ine! Mayo ine!”
Adzaitana alimi kuti alire,
Ndiponso akatswiri odziwa kulira maliro kuti alire mokweza.’
-