Amosi 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngakhale mutapereka nsembe zathunthu zopsereza ndiponso nsembe zoperekedwa ngati mphatso,Ine sindidzasangalala ndi nsembe zanuzo.+Ndipo sindidzakondwera ndi nsembe zanu zamgwirizano zanyama zonenepa.+
22 Ngakhale mutapereka nsembe zathunthu zopsereza ndiponso nsembe zoperekedwa ngati mphatso,Ine sindidzasangalala ndi nsembe zanuzo.+Ndipo sindidzakondwera ndi nsembe zanu zamgwirizano zanyama zonenepa.+