Amosi 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa Yehova ndi amene walamula,+Iye adzagwetsa nyumba zikuluzikulu moti zidzasanduka mulu wadothi.Ndipo nyumba zingʼonozingʼono zidzasanduka zibuma.+
11 Chifukwa Yehova ndi amene walamula,+Iye adzagwetsa nyumba zikuluzikulu moti zidzasanduka mulu wadothi.Ndipo nyumba zingʼonozingʼono zidzasanduka zibuma.+