Amosi 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mumasangalala ndi zinthu zopanda pake.Ndipo mukunena kuti: ‘Tapeza mphamvu patokha.’*+