Amosi 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, anandionetsa masomphenya awa: Ndinamuona akutumiza dzombe, mbewu zomaliza zitayamba kumera.* Zimenezi zinali mbewu zimene ankadzala, akamaliza kumweta udzu wopita kwa mfumu. Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:1 Nsanja ya Olonda,10/1/2007, tsa. 144/1/1989, ptsa. 22-23
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, anandionetsa masomphenya awa: Ndinamuona akutumiza dzombe, mbewu zomaliza zitayamba kumera.* Zimenezi zinali mbewu zimene ankadzala, akamaliza kumweta udzu wopita kwa mfumu.