Amosi 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dzombelo litamaliza kudya zomera zonse zamʼdziko, ine ndinati: “Inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, chonde khululukani.+ Kodi Yakobo apulumuka bwanji popeza ndi wofooka?”+
2 Dzombelo litamaliza kudya zomera zonse zamʼdziko, ine ndinati: “Inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, chonde khululukani.+ Kodi Yakobo apulumuka bwanji popeza ndi wofooka?”+