Amosi 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Yehova anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani Amosi?” Ndinamuyankha kuti: “Ndikuona chingwe chowongolera.” Ndiyeno Yehova anati: “Ndikuika chingwe chowongolera pakati pa anthu anga Aisiraeli, ndipo sindidzawakhululukiranso.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:8 Tsiku la Yehova, ptsa. 84-85 Nsanja ya Olonda,4/1/1989, tsa. 23
8 Ndiyeno Yehova anandifunsa kuti: “Kodi ukuona chiyani Amosi?” Ndinamuyankha kuti: “Ndikuona chingwe chowongolera.” Ndiyeno Yehova anati: “Ndikuika chingwe chowongolera pakati pa anthu anga Aisiraeli, ndipo sindidzawakhululukiranso.+