Amosi 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Amaziya wansembe wa ku Beteli,+ anatumiza uthenga kwa Yerobowamu+ mfumu ya Isiraeli wakuti: “Amosi akukukonzerani chiwembu mkati mwenimweni mwa Isiraeli,+ ndipo anthu atopa nawo mawu ake.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:10 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, tsa. 13
10 Ndiyeno Amaziya wansembe wa ku Beteli,+ anatumiza uthenga kwa Yerobowamu+ mfumu ya Isiraeli wakuti: “Amosi akukukonzerani chiwembu mkati mwenimweni mwa Isiraeli,+ ndipo anthu atopa nawo mawu ake.+