Amosi 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano imva zimene Yehova wanena, ‘Ukunena kuti: “Usanenere zinthu zoipa zokhudza Isiraeli,+ ndipo usanene mawu alionse+ oipa okhudza nyumba ya Isaki.”
16 Tsopano imva zimene Yehova wanena, ‘Ukunena kuti: “Usanenere zinthu zoipa zokhudza Isiraeli,+ ndipo usanene mawu alionse+ oipa okhudza nyumba ya Isaki.”