Amosi 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ‘Pa tsiku limenelo nyimbo za mʼkachisi zidzasanduka kulira mokweza,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Padzakhala mitembo yambiri yotayidwa paliponse+ moti kudzangoti zii!’
3 ‘Pa tsiku limenelo nyimbo za mʼkachisi zidzasanduka kulira mokweza,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Padzakhala mitembo yambiri yotayidwa paliponse+ moti kudzangoti zii!’